*[Verso 1]*
Ndipo kunali mazulo,
Davide anadzuka pakama,
Nayenda, nayenda,
Ndipo anaona nkazi akusamba.
*[Verso 2]*
Nkaziyo anali wokongola,
Ochititsa kaso, okongola,
Davide anatuma anthu,
Kukafunsira za nkaziyo.
*[Pre-Coro]*
Ndipo anagona naye,
Zosatira zake anatenga mimba,
Oh, anatenga mimba.
****
Davide, chifukwa chiyani?
Davide, mudachita chiyani?
Kutumiza uthenga kwa Yohabu,
Kuti Uriya apite kunkhondo.[Coro]
*[Verso 3]*
Anatumiza uthenga kwa Yohabu,
Asogole Uriya muhiti kunkhondo,
Cholinga akaphedwe,
Iye asale ndi nkaziyo.
*[Coro Final - Forte]*
Ooo Davideee,
Maso anawona kukongola,
Mtima unayiwala Mulungu,
Ndipo tchimo linabala imfa.
DJ Dax Six da moz