K Y O Malo achinyamata nthandizo la achinyamata lopezekelatu Malo omwe wachinyamata akafikako sabwelako chabe tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
Ngati uli ndi nkhawa tipeze ku Kawale Youth Organization ndipo nkhawa zonse zidzathawa ngati uli ndi mafunso okhudza ndi za sexual reproductive health rights bwela ku K Y O udzayankhidwa tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
ku kawale Youth Organization kuli achinyamata odziwa bwino kulandila achinyamata anzawo komaso anaphunzitsidwa mwa ukadaulo pothandiza anzawo odziwa kusunga chisinsi komanso ansangala pogwila ntchito yawo tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
Kawale Youth Organization ikupezeka ku Kawale Community Hospital mkati mwenimweni mwa chipatalachi mukafika mukapeza achina Triza, David, Emily, Linda, Joso, Chifundo, Upile, Edo, Hilda, Manesi Komaso Chief Apatsa azakulandilani mwansangala komaso kuli nyamata wantali bwino Gaza
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa
tiyeseni tiyeseni tiyeseni ndipo simudzakhumudwa tiyeseni