ndili kuno mawandukawumwa mowa umene ndawusowa *aphiri muli kuti nanga amalunga alikuti tiyeni tikatenge ndalama tikamwele mowa ndawusowa*.
*Bayala uli kuti._×4]
*Bwera undigule golide wanga!*
*ikakhala Business ndiye ikuyenda!*
Kasitomala ndineyo bayala uli kuti!*
*[Pre-Chorus]*
Anthu awa akundinena
"Uyu amakonda kuledzera"
Koma sakudziwa *magobo* omwe ndagwira
*Ku Madziku* ndidatopa
*[Chorus - Yaikulu]*
*MOWA WANGA NDI GOLIDE!*×2]
*NDAMPEZA NDI NTCHITO YAMMANJA!*
*BAYALA ULI KUTI? BWELA UNDIGULE!*
*BUSINESS IKUYENDA!*
*MUKUTI NDIKUMWA? AYI!*
*NDIKUMWA ZIPATSO ZA NTCHITO YANGA!*
*MOWA WANGA ulikuti.×3!*
*NDIDZIPESE NDIMWEKO!* 🍻
*[Verse 2]*
Ku *Chamba chafa* ndinakumbasoso
Kwa *Kachaso* ndinatopa
kwa *Tadzela nkhani* ndinagwiraso
Ndipo lero ndili pano ndikupuma
Mukuti ndimakonda kuledzera?
Ayi bwana, ndimakonda kupumula
Pambuyo pa ntchito yolimba
Ndi bwino kumwa mowa kusiyana ndi akazi
_**_
Ndidzipepese ndimweko
Thukuta langa ndimweko
Zipatso za ntchito ndimweko
Chifukwa ndinayenera[Bridge]
_**_
Bayala! Bayala!
Kasitomala wabwera!
Golide wasanduka ndalama!
*BUSINESS MAN*[Shout]
*[Chorus Yomaliza x4]*
*MOWA WANGA NDI GOLIDE!×4]
*NDAMPEZA NDI NTCHITO!*
*BAYALA ULI KUTI? BWELA UNDIGULE golide!*
*NDIDZIPESE NDIMWEKO!*
_**_
_Kwa odana nane... imwani nsanje zanuzo wanga ayi toto..._
_Kwa ine... ndimwa mowa wanga...*
*LOMA PANO ZIKUYENDA* 🔥💼[Outro]