[Intro]
Eeeee eeeeee
Oooooo eeeee
Mesa mesa aaaaaa
Eya mesa mesa aaaaa
Mesa akakondana alekeni
Eya mesa mesa aaaaaa
Mesa chichokondi ndi ndiawili
Eya mesa mesa aaaaaa
[Verse 1]
Nkati ndikusiye ndiwe hule
Umakonda ndalama
Ankati ndiwachimasomaso
Umafuna wahama
Koma iwe ndi ine shuwa
Eya mesa mesa aaaaaa
If we look at the world with a love of life, the world will reveal its beauty to us.
[Chorus]
Chikondi sichabwera ndi ndalama
Mtima wanga ukhoza kukuthandiza
Tidzakhalabe limodzi, mpaka kumapeto
Life is short to hate anyone so forgive often love someone smile often and do everything that makes you happy.
[Verse 2]
Happiness comes when you believe in what your doing, know what your doing, and love what you are doing.
Ngakhale fisi amakhala ndi bwezi
Bwezi lako ndine
Tachoka kutali
Eya kutili
[Chorus]
Chikondi sichabwera ndi ndalama
Koma Mumtima bwela love yokha ndikhuthulila
Tidzakhalabe limodzi, mpaka kumapeto
Eya limodzi mpaka kumapeto
[Outro]
Asanje alemba mmadza
Eya afufuta ndachule eya